Department of Climate Change and Meteorological Services
Department of Climate Change and Meteorological Services
February 15, 2025 at 01:54 PM
NYENGO YA USIKU UNO NDI MAWA PA 16 FEB 2025 ⛈️⛈️⛈️ ⛈️ Mvula ⚡Mphenzi Kukhala kwa chifunga mwapatalipatali komanso kugwa mvula m’madera ochepa am’zigawo za kum’mwera ndi pakati koma mvula ya mabingu ndi ya mphamvu igwa m’madera ena am’mphepete mwa nyanja ya Malawi ndi enanso am’chigawo cha kumpoto usiku uno ndi mawa m’mawa. ⛈️⛈️Mawa masana, tiyembekezere mvula ya mabingu ndi ya mphamvu kudzagwa m’madera ochulukirapo makamaka m’madera am’chigawo cha pakati ndi okwera. LANGIZO: Tipewe kuoloka madzi osefukira kapena omwe akuthamanga kwambiri. MPHEPO: Iziomba ya mkuntho m’madera omwe mukhale mabingu... ⛈️⛈️LOLEMBA: Tiyembekezere mvula yomwe idzagwe ya mphamvu m’madera ena...
👍 🙏 ❤️ 10

Comments