
Department of Climate Change and Meteorological Services
February 16, 2025 at 01:39 PM
NYENGO YA USIKU UNO NDI MAWA 17 FEB 2025
⛈️⛈️⛈️
⛈️ Mvula
⚡Mphenzi
Tiyembekezere mvula m’madera ochepa makamaka m’madera okwera komanso ena am’mphepete mwa nyanja ya Malawi usiku uno ndi mawa m’mawa.
⛈️⛈️Mawa masana, kudzakhala kwa mvula ya mabingu ndi ya mphamvu m’madera ochulukirapo makamaka m’madera okwera ndi enanso am’chigawo cha pakati.
LANGIZO: Osayendetsa galimoto m'madzi osefukira.
MPHEPO: Iziomba ya mkuntho m’madera omwe mukhale mabingu...
⛈️⛈️LACHIWIRI: Tiyembekezere mvula m’madera ambiri...
WhatsApp: https://whatsapp.com/channel/0029VaT21WW8PgsBmJWWGc1A
Website: https://www.metmalawi.gov.mw/products/daily-forecast/weather-forecast-16-february-2025/
🙏
👍
10