
ONLINE JOB VACANCIES
June 21, 2025 at 07:12 AM
Updates:
Date: Saturday, 21st June 2025
Time: 9:10am.
1) Walk-in Interviews for Multiple Positions_Recruitment of Health Care Workers, ma results ake aboma atulutsa dzulo Friday 20th June 2025 ndipo pdf yake tapanga post dzulo lomwelo. Tikatero imeneyi tathana nayo.
2) Interview ya *HSA, Statistical Clerk ndi Hospital Attendant,* ma results ake SANATUKE. Aboma akatulutsa ma results ake, tizalengeza pompa pa platform.
3) Kulemba ntchito aphunzitsi aku Primary, palipanopa tsiku loyamba kulemba komanso ndondomeko yake sanalengeze, dikirani ndithu ndipo aboma akalengeza tizapanga post pompa pa platform.
Idu Mwawa's Note:
Kindly share this post with others after reading.
Follow us on our WhatsApp Channel. Simply click the link below and tap the 'Follow Channel' button at the bottom of your screen.
https://whatsapp.com/channel/0029VaetCUH9sBIAoRxaLD14
Copyright © 2025 ONLINE JOB VACANCIES WhatsApp GROUP ✍🏻. Powered by Matcom Advertisement Agencies. All Rights Reserved.
👍
❤️
🙏
❤
👏
😢
46