Department of Climate Change and Meteorological Services
Department of Climate Change and Meteorological Services
February 2, 2025 at 12:00 PM
Expect rain of varying intensity over many areas, including several in the south, tomorrow, 3rd February, and Tuesday, 4th February 2025. Therefore, stay alert as *Flash Floods* are likely in floodprone areas such as lakeshore areas. Tiyembekezere mvula kugwa m'madera ambiri kuphatikizapo m'madera ochuluka am'chigawo chakumwera, mawa lino pa 3 February ndi Lachiwiri pa 4 February, 2025. Choncho, tikhale tcheru panthawiyi kuti tipewe kutaya miyoyo komanso katundu ku *madzi osefukira mwadzidzidzi* makamaka m'malo amene kumakonda kusefukira madzi monga m'madera am'mphepete mwa nyanja ya Malawi.
😢 👍 5

Comments