Department of Climate Change and Meteorological Services
February 7, 2025 at 12:27 PM
7 February, 2025
🌧️🌧️⚠️🌊
Expect rain of varying intensity over many areas tonight and tomorrow morning.
Expect rain over many areas tomorrow afternoon.
WARNING: The threat of flash floods is very high in vulnerable areas such Chikwawa and Nsanje. Therefore, stay alert and do not attempt to cross flooded or fast flowing water.
WINDS: variable but gusty in stormy areas…
FORECAST FOR SUNDAY: expect rainy weather to continue over more areas...
🌧️🌧️⚠️🌊
Tiyembekezere mvula ya mphamvu zosiyanasiyana kugwa m'madera ambiri usiku uno ndi mawa m’mawa.
Mawa masana, kudzakhala kwa nyengo ya mvula m’madera ambiri.
CHENJEZO: Chiopsezo cha kusefukira kwa madzi mwadzidzidzi ndi chokwera m’madera omwe madzi amasefukira kawirikawiri monga ku Chikwawa ndi ku Nsanje. Choncho, tikhale tcheru ndipo tipewe kuoloka madzi osefukira kapena othamanga kwambiri.
MPHEPO: Iziomba ya mkuntho m’madera omwe kukhale mabingu...
LAMULUNGU: Kudzakhala kwa nyengo ya mvula m’madera ambiri.
👍
🙏
❤️
12