Department of Climate Change and Meteorological Services
Department of Climate Change and Meteorological Services
February 8, 2025 at 02:16 PM
NYENGO YA USIKU UNO NDI MAWA PA 9 FEB 2025 🌧️🌧️⚠️🌊 Tiyembekezere mvula yomwe igwe ya mphamvu m’madera am’mphepete mwa nyanja ya Malawi usiku uno ndi mawa m’mawa. Mawa masana, kudzakhala kwa nyengo ya mvula m’madera ambiri. ⚠️🌊CHENJEZO: Chiopsezo cha kusefukira kwa madzi mwadzidzidzi ndi chokwera m’madera omwe madzi amasefukira kawirikawiri. Choncho, tikhale tcheru ndipo tipewe kuoloka madzi osefukira kapena othamanga kwambiri. MPHEPO: Iziomba ya mkuntho m’madera omwe kukhale mabingu... LOLEMBA: Kudzakhala kwa nyengo ya mvula m’madera ambiri.
👍 🙏 ❤️ 😂 😢 22

Comments