Department of Climate Change and Meteorological Services
                                
                            
                            
                    
                                
                                
                                February 9, 2025 at 02:08 PM
                               
                            
                        
                            NYENGO YA USIKU UNO NDI MAWA PA 10 FEB 2025
🌧️ 🌧️ 
Mvula ikuyembekezeka kugwa m’madera ochepa makamaka am’mphepete mwa nyanja ya Malawi usiku uno ndi mawa m’mawa. 
Mawa masana, kudzakhala kwa mitambo komanso kudzatentha ndipo mvula ya mabingu idzagwa m’madera ochepa makamaka m’madera okwera ndi ena am’chigawo cha pakati.
LANGIZO:  Tipewe kuoloka madzi osefukira kapena omwe akuthamanga kwambiri.
🌧️ 🌧️ LACHIWIRI: Kudzagwa mvula ya mphamvu m’madera ambiri.
                        
                    
                    
                    
                    
                    
                                    
                                        
                                            👍
                                        
                                    
                                        
                                            🙏
                                        
                                    
                                        
                                            ❤️
                                        
                                    
                                    
                                        11