
Department of Climate Change and Meteorological Services
February 14, 2025 at 11:46 AM
NYENGO YA USIKU UNO NDI MAWA PA 15 FEB 2025
⛈️⛈️⛈️
⛈️ Mvula
⚡Mphenzi
Kukhala kwa mitambo komanso kufunda ndipo mvula ya mabingu igwa m’madera ena makamaka am’mphepete mwa nyanja ya Malawi usiku uno ndi mawa m’mawa.
⛈️⛈️Mawa masana, tiyembekezere mvula ya mabingu kudzagwa m’madera ochulukirapo am’zigawo za kum’mwera ndi pakati.
LANGIZO: Tipewe kuoloka madzi osefukira kapena omwe akuthamanga kwambiri.
MPHEPO: Iziomba ya mkuntho m’madera omwe mukhale mabingu...
⛈️⛈️LAMULUNGU: Tiyembekezere mvula yomwe idzagwe ya mphamvu m’madera ena...
👍
🙏
11