Department of Climate Change and Meteorological Services
Department of Climate Change and Meteorological Services
February 18, 2025 at 01:07 PM
NYENGO YA USIKU UNO NDI MAWA 19 FEB 2025 ⛈️⛈️⛈️ ⛈️ Mvula ⚡Mphenzi ⛈️⛈️Tiyembekezere mvula m’madera ochepa makamaka am’mphepete mwa nyanja ya Malawi usiku uno ndi mawa m’mawa. ⛈️⛈️Mawa masana, m’madera ambiri, kuphatikizapo m’madera ochuluka am’chigawo cha kumpoto, akuyembekezeka kudzalandira mvula yochuluka. LANGIZO: Chiopsezo chakusefukira kwa madzi mwadzidzidzi ndi chokwera m’madera omwe madzi amasefukira kawirikawiri. Choncho, tikhale tcheru ndipo tipewe kuoloka madzi osefukira kapena othamanga kwambiri. MPHEPO: Iziomba ya mkuntho m’madera omwe mukhale mabingu... ⛈️⛈️LACHINAYI:Tiyembekezere mvula kudzapitirira kugwa m’madera ambiri....
👍 🙏 ❤️ 😮 6

Comments