
Department of Climate Change and Meteorological Services
February 20, 2025 at 03:53 PM
#zbsnews
Mlatho wa Mpiri omwe uli pansewu wa Bakili Muluzi Highway pakati pa Chiponde komanso Liwonde m'boma la Machinga wagumukira.
Malinga ndi m'neneri wa apolisi m'bomali, a Western Kansire, mlathowu wagumukira kaamba ka mvula yamphamvu yomwe yakhala ikugwa m'bomali.
Iwo ati mbali zonse za msewuwu azitseka pofuna kupewa ngozi.
(by Eamon Piringu - Lilongwe:02/19/2025)
#malawismostfollowedpage
😢
👍
😮
🙏
15