Malawi Job Vacancies and adverts
February 26, 2025 at 10:35 AM
Kungoitanidwa ku ma interview ku Thyolo District Council nthawi yomweyo ku inbox kwangozaza ndi mafuso ati kodi HSA amalandila zingati
Guys, it's not over yet. Focus kae za ma interview, HSA apart from salary kuli tizochitikachitika tambili tobwelesa ndalama.
Pray, do research about ma interview kuti amabwela motani, you can ask amene anapangapo kale kuti zimabwela motani because mafuso ake samasiyana kwenikweni
Mafuno abwino kwa nonse amene mwaitanidwa ku ma interview malo osiyanasiyana
Osaiwala kupanga check email amene munalembela za internship ya NBS, akumatumiza link kumeneko ya aptitude test. Only one attempt, once you mess up you are done
👍
😂
🙌
10