
Department of Climate Change and Meteorological Services
May 14, 2025 at 07:54 AM
Mphepo ya Chiperoni yomwe ikuomba mdziko muno itionetsa zinthu.
Mwachitsanzo anthu ambiri m'township ya Limbe, anavala mawovololo akuchipatala otchedwa kuti coverall interfaces.
Awa ndi ma ovololo omwe ankapezeka kwambiri ndi anthu za achipatala munyengo ya muliri wa Covid 19.
Pano zovalazi zikugulitsidwa pa mitengo ya K 3,500- kulekeza K4,000.
Padakali pano, nthambi ya nyengo yati mphepoyi ichepa mphamvu lachinayi lino.
#mijnews #malawinews #malawi
-Nicolas Mbonela-

😂
👍
😢
❤️
🙏
46