
Department of Climate Change and Meteorological Services
May 14, 2025 at 01:25 PM
NYENGO YA USIKU UNO NDI MAWA PA 14 MAY 2025
🌧
Tiyembekezere nyengo ya Chiperoni yomwe ndi nyengo ya mvula, ya mphepo, ya mitambo yambiri ndi yozizira komanso ya chifunga kudzayamba kuchepa mphamvu mawa lino pa 15 May 2025.
🌊⚠️CHENJEZO: Mphepo ya Mwera ya liwiro loposa 50km/h ikuyembekezeka kupitilira kuomba pa nyanja zathu monga nyanja ya Malawi ndi nyanja zina. Mphepoyi ikuyekezeka kuyamba kuchepa mphamvu kuyambira mawa lino pa 15 May 2025. Ngakhale zili choncho, tikulimbikitsabe onse omwe amagwiritsa ntchito nyanjazi kuti akapitilize kukhala osamala.
MPHEPO: Iziomba kuchokera kum’mwera cha kumvuma...
Facebook: https://web.facebook.com/MetMalawiDCCMS
Website: https://www.metmalawi.gov.mw/products/daily-forecast/weather-forecast-15-may-2025/

❤️
3