
Department of Climate Change and Meteorological Services
May 15, 2025 at 07:18 AM
15 May 2025
🌦🌤⛅️🌤
Nyengo ya Chiperoni ndiye yachepa mphamvu Kum'mwera ndi pakati , zikatero Mphepo ya Mwera pa nyanja ichepanso mphamvu. Koma nyengo ya Mvula ipitirira m'madera ena am'chigawo cha kumpoto.
Facebook: https://web.facebook.com/MetMalawiDCCMS
Photo Credit: Malawi Weather Chasers (Place: Mponela, Dowa)

👍
❤️
😂
🙏
13