Department of Climate Change and Meteorological Services
                                
                            
                            
                    
                                
                                
                                May 15, 2025 at 11:14 AM
                               
                            
                        
                            NYENGO YA USIKU UNO NDI MAWA PA 16 MAY 2025
🌤🌧🌊
Tiyembekezere nyengo yozizira m’madera ambiri koma mvula igwa m’madera ochepa makamaka am’chigawo cha kumpoto usiku uno ndi mawa m’mawa.
Mawa masana, kudzakhala kwa nyengo ya mitambo yapatalipatali ndipo kudzafunda koma mvula idzagwa m’madera ochepa.
🌬🌊LANGIZO: Pomwe Mphepo ya Mwera ikuchepa mphamvu, anthu omwe amagwiritsa ntchito nyanja zathu monga asodzi, akulimbikitsidwa kukhalabe osamala mpaka panyanja patakhala pa bata.  
Mphepo: Iziomba mochokera kum’mwera cha kumvuma...
Loweruka: Kudzakhala kwa mitambo komanso kudzafunda...
Facebook: https://web.facebook.com/MetMalawiDCCMS
Website: https://www.metmalawi.gov.mw/products/daily-forecast/weather-forecast-16-may-2025/
                        
                    
                    
                    
                        
                        
                                    
                                        
                                            👍
                                        
                                    
                                        
                                            ❤️
                                        
                                    
                                    
                                        6