
Department of Climate Change and Meteorological Services
May 16, 2025 at 02:09 PM
NYENGO YA USIKU UNO NDI MAWA PA 17 MAY 2025
🌤🌧
Tiyembekezere nyengo yozizira m’madera ambiri koma kukhala kwa chifunga komanso kugwa mvula m’madera ochepa am’chigawo cha kumpoto usiku uno ndi mawa m’mawa.
Mawa masana, kudzakhala kwa nyengo ya mitambo yapatalipatali ndipo kudzafunda koma mvula idzagwa m’madera ochepa makamaka m’madera okwera ndi am’mphepete mwa nyanja ya Malawi ku chigawo chakumpoto.
LANGIZO: Tisagone ndi mbaula yoyaka mnyumba kuopa kufera kutulo.
MPHEPO: Iziomba mochokera kum’mwera cha kumvuma...
LAMULUNGU: Kudzakhala kwa mitambo yapatalipatali komanso kudzafunda...
Facebook: https://web.facebook.com/MetMalawiDCCMS
Website: https://www.metmalawi.gov.mw/products/daily-forecast/weather-forecast-17-may-2025/

🙏
1