
Department of Climate Change and Meteorological Services
May 29, 2025 at 06:57 AM
Usiku wathawu ndi lero m'mawa pa 29 May 2025 kunazizira chonchi m'madera ena.
Kamuzu International Airport 11°C
Bvumbwe 11°C
Chichiri Blantyre 12°C
Kasungu 13°C
Mzimba 14°C
Ntaja Machinga 15°C
Mzuzu 16°C
Ngabu Chikwawa 17°C
1. Tikumbukire kuvala za mphepo
2. Tisagone ndi mbaula yoyaka m'nyumba kuopa kufera kutulo
3. Anthu omwe ali ndi vuto la Mphumu/Asthma akupemphedwa kukhala osamalitsa.
👍
😢
🙏
5