Department of Climate Change and Meteorological Services
June 7, 2025 at 12:20 PM
M’mene nyengo ikhalire usiku uno ndi mawa pa 8 June 2025
⛅️⛅️⛅️Tiyembekezere nyengo ya mitambo yapatali patali ndi yofunda usiku uno ndi mawa m’mawa.
Mawa masana, kudzakhala kwa nyengo ya mitambo yapatalipatali, yamphepo ndi yotentha m’madera ambiri.
MPHEPO: Iziomba mochokera kum’mwera chakumvuma...
LOLEMBA: Tiyembekezere nyengo ya mitambo yapatalipatali ndi mphepo...
👍
🙏
9