Department of Climate Change and Meteorological Services
Department of Climate Change and Meteorological Services
June 11, 2025 at 10:09 AM
NYENGO YA USIKU UNO NDI MAWA PA 12 JUNE 2025 Usiku uno ndi mawa m’mawa, tiyembekezere nyengo ya mphepo, ya fumbi, ya mitambo, yozizira ndi ya chifunga mwapatalipatali komanso ya mvula yamawawa. Mawa masana, kudzakhala kwa nyengo ya mphepo, ya mitambo ndi ya chifunga mwapatalipatali ndipo kudzagwanso mvula yamawawa m’madera ena makamaka m’madera okwera ndi am’mphepete mwa nyanja ya Malawi. ⚠️🌊CHENJEZO: Mphepo ya mphamvu ya Mwera ikuyembekezeka kuomba pa nyanja zathu monga pa nyanja ya Malawi kuyambira lero Lachitatu pa 11 June 2025 ndipo idzachepa mphamvu lolemba pa 16 June 2025. Choncho, tikhale tcheru komanso osamala kuti titeteze miyoyo ndi katundu. MPHEPO: Iziomba mwamphamvu ndipo mochokera kum’mwera chakumvuma... ☁️LACHISANU: Tiyembekezere nyengo ya Chiperoni... Facebook: https://web.facebook.com/MetMalawiDCCMS Formore: https://www.metmalawi.gov.mw/products/daily-forecast/weather-forecast-12-june-2025/
Image from Department of Climate Change and Meteorological Services: NYENGO YA  USIKU UNO NDI MAWA PA 12 JUNE 2025  Usiku uno ndi mawa m’ma...

Comments