
Department of Climate Change and Meteorological Services
June 12, 2025 at 09:19 AM
NYENGO YA USIKU UNO NDI MAWA PA 13 JUNE 2025
Usiku uno ndi mawa m’mawa, tiyembekezere nyengo ya Chiperoni yomwe ndi nyengo ya mphepo, ya fumbi, ya mitambo, yozizira ndi ya chifunga mwapatalipatali komanso ya mvula yamawawa koma mvula ya mphamvu igwa m’madera ena am’chigawo cha kumpoto monga ku Mzuzu, ku Nkhatabay ndi ku Karonga.
Mawa masana, kudzakhala kwa nyengo ya Chiperoni m’madera ambiri.
⚠️🌬🌊CHENJEZO: Mphepo ya mphamvu ya Mwera ikuomba pa nyanja zathu monga pa nyanja ya Malawi ndipo idzachepa mphamvu pofika Lolemba pa 16 June 2025. Choncho, tikhale tcheru komanso osamala kuti titeteze miyoyo ndi katundu.
MPHEPO: Iziomba mwamphamvu ndipo mochokera kum’mwera chakumvuma...
LOWERUKA: Tiyembekezere nyengo ya Chiperoni...
Formore: https://www.metmalawi.gov.mw/products/daily-forecast/weather-forecast-13-june-2025/

👍
1