
Capital FM Malawi
May 30, 2025 at 07:49 AM
Bungwe loona za misewu lero likukhazikitsa ndondomeko yamomwe ntchito zachitukuko chamisewu ziyendere kuyambira chaka chino mpaka chaka cha 2030.
Mwambowu omwe ukuchitikira mumzinda wa Lilongwe wayamba ndi ulendo wandawala wamtunda pafupifupi makilomita awiri kupita kumalo omwe mwambo waukulu uuchitikire ku ku Bingu International Convention Center-BICC.
Wolemba ndi kujambula: Joseph Mazizi
#cfmnews
#malawi
👍
🙏
5