Capital FM Malawi
Capital FM Malawi
June 6, 2025 at 12:26 PM
#breaking Wachiwiri kwa nduna ya maboma aang’ono, umodzi ndi chikhalidwe, Joyce Chitsulo wamwalira. Tikupatsirani zambiri za nkhaniyi. #cfmnews #malawi
😢 😭 😮 🙏 18

Comments