Capital FM Malawi
Capital FM Malawi
June 9, 2025 at 05:53 AM
Mtsogoleri wa dziko lino, Lazarus Chakwera lero akhala nawo pa mwambo oyika m'manda thupi la yemwe anali wachiwiri kwa nduna ya maboma aang'ono, Joyce Chitsulo. Chitsulo, yemwenso anali phungu wa dera la ku madzulo kwa boma la Mwanza, wamwalira lachisanu sabata yatha. #cfmnews #malawi
😭 ❤️ 😢 🤓 5

Comments